DRIEMO COMPENSATION Lyrics video











>> YOUR LINK HERE: ___ http://youtube.com/watch?v=_ZCoG6BgSvc

Intro • Kuti mwina compensation • Driemo • Ndidzapereke moyo wanga • Verse1 • Oh mtima uwupereke, kwaine ndiwutenge • Don't you worry about safety • Ndidzachengetera chengetera chengetera • I know mtima unaswekapo • You've been there unalirapo, ululu mumtima kufikapo • Ukaganizira ganizira ganizira • Paiwe ndilola ndipepere, chikondi chisaperewere • Olo pa ground paterere I will love you the same baby • Hook • Oh udzandifunse • Ndikadzakuswera mtima udzandifunse • Kuti mwina compensation • Ndidzapereke moyo wanga x2 • Verse2 • Don't be scared to love me more • Zakale zapita it's me and you • Undiuze pomwe Pali mantha ako • • I know mtima umakana ukandiunika • Umaona ngati Aja anakunamiza koma • I wanna be your soldier • Your fighter • Protector • Defender • I just wanna be your friend for life • Hook • Oh udzandifunse • Ndikadzakuswera mtima udzandifunse • Kuti mwina compensation • Ndidzapereke moyo wanga x2 • Bridge • Ooh udzandifunse • Udzandifunse, mwina compensation ndidzapereke moyo wanga eeee • Hook • Oh udzandifunse • Ndikadzakuswera mtima udzandifunse • Kuti mwina compensation • Ndidzapereke moyo wanga x2 • Tags • COMPENSATION, DRIEMO, VAN NGONGO, VJ KEN, RON CZ, 8MEDIA • #DRIEMO #compensation #LYRICOZMmuziq

#############################









New on site
Content Report
Youtor.org / YTube video Downloader © 2025

created by www.youtor.org